WIRE โ€” Apolisi a kwa Jenda ku Mzimba Lachisanu adamanga a Ras David Chikomeni Chirwa, a zaka 49 powaganizira kuti adapezeka ndi makilogalamu 19.2 a chamba popanda chilolezo. Iwowa ndi mmodzi mwa akuluakulu amene ali mu board yoyendetsa nthambi ya boma yoyang'anira ulimi wa chamba chovomerezeka chimene si chozunguza bongo ya Cannabis Regulatory Authority (CRA). Apolisi adamanga The post Amanga a Chikomeni pa za chamba appeared first on Nation Online.

"We aggregate wires to encourage regional discovery, sending readers directly back to the original source to explore full coverage."

This is a normalized overview of the breaking feed event. The complete, official release detailing all points, background context, and statements remains hosted by the original publisher.