WIRE โ€” Bwalo la majisitileti ku Zomba lachisanu lidagamula Senior Chief Malemia kuti akakhale ku ndende zaka 21 pa mlandu wogonana ndi mtsikana wachichepere komanso kuthandizira kuchotsa mimba. Popereka chilangocho, woweruza a Elijah Daniels, pa mlandu woyamba adapereka zaka 21 pamene mlandu wachiwiri zaka 9, zonse 30. Koma a Daniels adauza bwalolo kuti achotsera zaka 9 chifukwa

"We aggregate wires to encourage regional discovery, sending readers directly back to the original source to explore full coverage."

This is a normalized overview of the breaking feed event. The complete, official release detailing all points, background context, and statements remains hosted by the original publisher.