WIRE โ€” Nduna ya za chuma, mapulani a za chuma, komanso kupereka mphamvu ku anthu a Joseph Mwanamvekha yati boma lapereka K100 biliyoni zogulira chimanga ku nthambi ya National Food Reserve Agency (NFRA). Poyankhula m'Nyumba ya Malamulo mkati mwa sabatayi, a Mwanamvekha anati ndalamazo ndi gawo la ntchito yolimbikitsa chitetezo cha chakudya m'dziko muno pamene akatswiri akulosera The post Boma lapereka K100biliyoni yogulira chimanga appeared first on Nation Online.

"We aggregate wires to encourage regional discovery, sending readers directly back to the original source to explore full coverage."

This is a normalized overview of the breaking feed event. The complete, official release detailing all points, background context, and statements remains hosted by the original publisher.