WIRE โ€” Nzika zokhudzidwa ku Liwonde m'boma la Machinga zaopsedza kuti ziletsa kuyamba kwa ntchito yokonzanso msewu wa Liwonde-Matawale (M003) pokhapokha boma litawunikanso ndalama za chipukuta misozi zomwe likupereka kwa anthu okhudzidwa ndi ntchitoyi. Ntchito yokonza nsewuwu, omwe ndi wa ma kilomita 47 ndi ndalama pafupifupi K101 billion zomwe zikupelekedwa ndi bank yaikulu pa dziko la pansi The post Chipepeso kaye musanayambe mseu appeared first on Nation Online.

"We aggregate wires to encourage regional discovery, sending readers directly back to the original source to explore full coverage."

This is a normalized overview of the breaking feed event. The complete, official release detailing all points, background context, and statements remains hosted by the original publisher.